Ekisodo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndi mulungu uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+ Mumasonyeza kuti ndinu woyera koposa,+ ndani angafanane ndi inu? Ndinu woyenera kuopedwa ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda. Inu mumachita zodabwitsa.+ Salimo 83:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anthu adziwe kuti inu, amene dzina lanu ndinu Yehova,+Inu nokha ndinu Wamʼmwambamwamba, woyenera kulamulira dziko lonse lapansi.+
11 Ndi mulungu uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+ Mumasonyeza kuti ndinu woyera koposa,+ ndani angafanane ndi inu? Ndinu woyenera kuopedwa ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda. Inu mumachita zodabwitsa.+
18 Anthu adziwe kuti inu, amene dzina lanu ndinu Yehova,+Inu nokha ndinu Wamʼmwambamwamba, woyenera kulamulira dziko lonse lapansi.+