2 Samueli 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako anaika Likasa la Yehova pamalo ake mutenti imene Davide anamanga.+ Ndiyeno Davide anapereka kwa Yehova+ nsembe zopsereza+ ndi nsembe zamgwirizano.+ 2 Samueli 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno mfumuyo inauza mneneri Natani+ kuti: “Ine ndikukhala mʼnyumba ya mitengo ya mkungudza,+ pamene Likasa la Mulungu woona likukhala mutenti.”+
17 Kenako anaika Likasa la Yehova pamalo ake mutenti imene Davide anamanga.+ Ndiyeno Davide anapereka kwa Yehova+ nsembe zopsereza+ ndi nsembe zamgwirizano.+
2 Ndiyeno mfumuyo inauza mneneri Natani+ kuti: “Ine ndikukhala mʼnyumba ya mitengo ya mkungudza,+ pamene Likasa la Mulungu woona likukhala mutenti.”+