-
1 Samueli 13:13, 14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Koma Samueli anauza Sauli kuti: “Zimene wachitazi ndi zopusa. Sunamvere lamulo limene Yehova Mulungu wako anakupatsa.+ Ukanamvera, Yehova akanachititsa kuti banja lako lilamulire Isiraeli mpaka kalekale. 14 Koma tsopano ufumu wako sukhalitsa.+ Yehova apeza munthu wapamtima pake,+ ndipo Yehova amuika kukhala mtsogoleri wa anthu ake+ chifukwa iwe sunamvere zimene Yehova anakulamula.”+
-