Mlaliki 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komanso chikondi chawo, chidani chawo ndi nsanje yawo zatha kale, ndipo alibenso gawo lililonse pa zimene zikuchitika padziko lapansi pano.+
6 Komanso chikondi chawo, chidani chawo ndi nsanje yawo zatha kale, ndipo alibenso gawo lililonse pa zimene zikuchitika padziko lapansi pano.+