-
2 Samueli 13:12-14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Koma Tamara anamuuza kuti: “Ayi, achimwene! Musandichititse manyazi, chifukwa zoterezi sizinachitikepo mu Isiraeli.+ Musachite zinthu zochititsa manyazi ngati zimenezi.+ 13 Kodi ine ndizikhala bwanji zimenezi zikachitika? Komanso Aisiraeli azikuonani ngati munthu woipa komanso wochititsa manyazi. Lankhulani ndi mfumu, chifukwa sangakukanizeni kuti munditenge.” 14 Koma Aminoni sanamumvere ndipo popeza anali ndi mphamvu kuposa Tamarayo, anamugwiririra.
-