2 Samueli 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Ahimazi+ mwana wa Zadoki anati: “Bwanji ndithamange ndikapereke uthengawu kwa mfumu, chifukwa Yehova wachitira mfumu chilungamo poilanditsa mʼmanja mwa adani ake?”+
19 Ndiyeno Ahimazi+ mwana wa Zadoki anati: “Bwanji ndithamange ndikapereke uthengawu kwa mfumu, chifukwa Yehova wachitira mfumu chilungamo poilanditsa mʼmanja mwa adani ake?”+