Ekisodo 22:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Usatemberere* Mulungu+ kapena mtsogoleri* amene ali pakati pa anthu a mtundu wako.+ Mlaliki 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ngakhale mʼmaganizo mwako,* usatemberere* mfumu+ ndipo usatemberere munthu wolemera kuchipinda kwako. Chifukwa mbalame* ikhoza kutenga mawu ako* kapena cholengedwa chokhala ndi mapiko chikhoza kukaulula zimene wanenazo.
20 Ngakhale mʼmaganizo mwako,* usatemberere* mfumu+ ndipo usatemberere munthu wolemera kuchipinda kwako. Chifukwa mbalame* ikhoza kutenga mawu ako* kapena cholengedwa chokhala ndi mapiko chikhoza kukaulula zimene wanenazo.