17 Ndiyeno Ahitofeli anauza Abisalomu kuti: “Bwanji ndisankhe amuna 12,000 kuti usiku uno ndikasakesake Davide? 2 Ndikamupeza atatopa komanso alibe mphamvu+ ndipo ndikamupanikiza. Zikakatero, anthu onse amene ali naye akathawa ndipo ine ndikapha mfumu yokhayo.+