Levitiko 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Usamayendeyende pakati pa anthu a mtundu wako nʼkumafalitsa miseche.+ Usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako.*+ Ine ndine Yehova. 2 Samueli 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako mfumu inafunsa kuti: “Nanga mwana* wa mbuye wako ali kuti?”+ Ziba anauza mfumu kuti: “Watsala ku Yerusalemu ndipo wanena kuti, ‘Lero nyumba ya Isiraeli indibwezera ufumu wa bambo anga.’”+
16 Usamayendeyende pakati pa anthu a mtundu wako nʼkumafalitsa miseche.+ Usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako.*+ Ine ndine Yehova.
3 Kenako mfumu inafunsa kuti: “Nanga mwana* wa mbuye wako ali kuti?”+ Ziba anauza mfumu kuti: “Watsala ku Yerusalemu ndipo wanena kuti, ‘Lero nyumba ya Isiraeli indibwezera ufumu wa bambo anga.’”+