Genesis 50:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ana akewo anamunyamula nʼkupita naye kudziko la Kanani ndipo anakamuika mʼphanga mʼmunda wa Makipela, umene uli moyangʼanizana ndi munda wa Mamure. Mundawo ndi umene Abulahamu anagula kwa Efuroni, Muhiti, kuti akhale manda.+
13 Ana akewo anamunyamula nʼkupita naye kudziko la Kanani ndipo anakamuika mʼphanga mʼmunda wa Makipela, umene uli moyangʼanizana ndi munda wa Mamure. Mundawo ndi umene Abulahamu anagula kwa Efuroni, Muhiti, kuti akhale manda.+