Ekisodo 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pa tsiku lachitatu mʼmawa, kunachita mabingu ndi mphezi ndipo mtambo wakuda+ unakuta phiri. Kunamvekanso kulira kwamphamvu kwambiri kwa lipenga la nyanga ya nkhosa, moti anthu onse mumsasawo anayamba kunjenjemera.+ 1 Samueli 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova adzawononga onse olimbana naye,*+Akadzawakwiyira, kumwamba kudzagunda mabingu.+ Yehova adzaweruza dziko lonse lapansi,+Iye adzapereka mphamvu kwa mfumu yake,+Ndipo adzakweza nyanga* ya wodzozedwa wake.”+
16 Pa tsiku lachitatu mʼmawa, kunachita mabingu ndi mphezi ndipo mtambo wakuda+ unakuta phiri. Kunamvekanso kulira kwamphamvu kwambiri kwa lipenga la nyanga ya nkhosa, moti anthu onse mumsasawo anayamba kunjenjemera.+
10 Yehova adzawononga onse olimbana naye,*+Akadzawakwiyira, kumwamba kudzagunda mabingu.+ Yehova adzaweruza dziko lonse lapansi,+Iye adzapereka mphamvu kwa mfumu yake,+Ndipo adzakweza nyanga* ya wodzozedwa wake.”+