1 Samueli 26:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova ndi amene adzabwezera aliyense mogwirizana ndi chilungamo chake+ komanso kukhulupirika kwake. Lero Yehova anakuperekani mʼmanja mwanga, koma sindinafune kuvulaza wodzozedwa wa Yehova.+ 1 Mafumu 8:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 inu mumve muli kumwamba ndipo muchitepo kanthu posonyeza amene ali wolakwa nʼkumubwezera mogwirizana ndi zochita zake komanso musonyeze amene ali wosalakwa nʼkumupatsa mphoto mogwirizana ndi chilungamo chake.+
23 Yehova ndi amene adzabwezera aliyense mogwirizana ndi chilungamo chake+ komanso kukhulupirika kwake. Lero Yehova anakuperekani mʼmanja mwanga, koma sindinafune kuvulaza wodzozedwa wa Yehova.+
32 inu mumve muli kumwamba ndipo muchitepo kanthu posonyeza amene ali wolakwa nʼkumubwezera mogwirizana ndi zochita zake komanso musonyeze amene ali wosalakwa nʼkumupatsa mphoto mogwirizana ndi chilungamo chake.+