Yesaya 44:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova, Mfumu ya Isiraeli,+ amene anawawombola,+Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, wanena kuti: ‘Ine ndine woyamba ndi womaliza.+ Ndipo palibenso Mulungu wina kupatulapo ine.+
6 Yehova, Mfumu ya Isiraeli,+ amene anawawombola,+Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, wanena kuti: ‘Ine ndine woyamba ndi womaliza.+ Ndipo palibenso Mulungu wina kupatulapo ine.+