1 Samueli 30:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Davide anali ndi nkhawa kwambiri chifukwa anthu ankakambirana zoti amuponye miyala. Anthuwo ankafuna kuchita zimenezi chifukwa anakwiya kwambiri ndi kutengedwa kwa ana awo aamuna ndi aakazi. Koma Davide anakhulupirira Yehova Mulungu wake ndipo anapeza mphamvu.+ 2 Samueli 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komanso pamene Abisalomu ankapereka nsembe, anaitanitsa Ahitofeli+ wa ku Gilo, mlangizi wa Davide,+ kuchoka kumzinda wakwawo wa Gilo.+ Anthu amene anagwirizana ndi Abisalomu pa chiwembuchi anapitiriza kuwonjezeka.+
6 Davide anali ndi nkhawa kwambiri chifukwa anthu ankakambirana zoti amuponye miyala. Anthuwo ankafuna kuchita zimenezi chifukwa anakwiya kwambiri ndi kutengedwa kwa ana awo aamuna ndi aakazi. Koma Davide anakhulupirira Yehova Mulungu wake ndipo anapeza mphamvu.+
12 Komanso pamene Abisalomu ankapereka nsembe, anaitanitsa Ahitofeli+ wa ku Gilo, mlangizi wa Davide,+ kuchoka kumzinda wakwawo wa Gilo.+ Anthu amene anagwirizana ndi Abisalomu pa chiwembuchi anapitiriza kuwonjezeka.+