2 Samueli 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Davide anadziwa kuti Yehova wachititsa kuti ufumu wake ukhazikike mu Isiraeli,+ komanso kuti ukhale wamphamvu+ chifukwa cha anthu a Mulungu, Aisiraeli.+ 2 Samueli 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ine ndidzakhala nawe kulikonse kumene ungapite,+ ndipo ndidzagonjetsa adani ako onse pamaso pako.+ Ndidzachititsa kuti dzina lako lidziwike+ ngati mmene zimakhalira ndi anthu otchuka mʼdzikoli.
12 Davide anadziwa kuti Yehova wachititsa kuti ufumu wake ukhazikike mu Isiraeli,+ komanso kuti ukhale wamphamvu+ chifukwa cha anthu a Mulungu, Aisiraeli.+
9 Ine ndidzakhala nawe kulikonse kumene ungapite,+ ndipo ndidzagonjetsa adani ako onse pamaso pako.+ Ndidzachititsa kuti dzina lako lidziwike+ ngati mmene zimakhalira ndi anthu otchuka mʼdzikoli.