Numeri 16:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Kenako Mose anauza Aroni kuti: “Tenga chofukizira ndipo uikemo moto wochokera paguwa lansembe.+ Uikemonso nsembe yofukiza nʼkupita kwa anthuwo mofulumira kuti ukawaphimbire machimo awo.+ Chita zimenezi chifukwa Yehova wakwiya kwambiri ndipo mliri wayamba kale!” 1 Mbiri 27:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Yowabu mwana wa Zeruya anayamba kuwerenga anthu koma sanamalize. Ndipo Mulungu anakwiyira kwambiri Aisiraeli chifukwa chowerenga anthuwo,+ moti chiwerengerocho sichinalembedwe mʼmbiri ya zochitika za nthawi ya Mfumu Davide.
46 Kenako Mose anauza Aroni kuti: “Tenga chofukizira ndipo uikemo moto wochokera paguwa lansembe.+ Uikemonso nsembe yofukiza nʼkupita kwa anthuwo mofulumira kuti ukawaphimbire machimo awo.+ Chita zimenezi chifukwa Yehova wakwiya kwambiri ndipo mliri wayamba kale!”
24 Yowabu mwana wa Zeruya anayamba kuwerenga anthu koma sanamalize. Ndipo Mulungu anakwiyira kwambiri Aisiraeli chifukwa chowerenga anthuwo,+ moti chiwerengerocho sichinalembedwe mʼmbiri ya zochitika za nthawi ya Mfumu Davide.