-
Miyambo 3:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Wosangalala ndi munthu amene amapeza nzeru,+
Ndiponso munthu amene amaphunzira zinthu zimene zingamuthandize kukhala wozindikira.
-
Miyambo 3:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Mʼdzanja lake lamanja muli moyo wautali.
Mʼdzanja lake lamanzere muli chuma ndi ulemerero.
-
-
-