1 Mafumu 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kuzungulira mʼkhosi mwake monse munali zokongoletsera zooneka ngati zipanda.+ Pamalo alionse otalika mkono umodzi ankaikapo zokongoletsera 10. Zokongoletsera zooneka ngati zipandazo zinalipo mizere iwiri, ndipo anaziumbira kumodzi ndi thankiyo.
24 Kuzungulira mʼkhosi mwake monse munali zokongoletsera zooneka ngati zipanda.+ Pamalo alionse otalika mkono umodzi ankaikapo zokongoletsera 10. Zokongoletsera zooneka ngati zipandazo zinalipo mizere iwiri, ndipo anaziumbira kumodzi ndi thankiyo.