1 Mafumu 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa nthawi imeneyi Adoniya+ mwana wa Hagiti anayamba kudzikweza nʼkumanena kuti: “Ineyo ndikhala mfumu!” Iye anapangitsa galeta ndipo anali ndi amuna okwera pamahatchi* komanso amuna 50 oti azithamanga patsogolo pake.+ 1 Mafumu 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anagwirizana ndi Yowabu mwana wa Zeruya komanso wansembe Abiyatara+ ndipo awiriwa anayamba kumutsatira komanso kumuthandiza.+
5 Pa nthawi imeneyi Adoniya+ mwana wa Hagiti anayamba kudzikweza nʼkumanena kuti: “Ineyo ndikhala mfumu!” Iye anapangitsa galeta ndipo anali ndi amuna okwera pamahatchi* komanso amuna 50 oti azithamanga patsogolo pake.+
7 Iye anagwirizana ndi Yowabu mwana wa Zeruya komanso wansembe Abiyatara+ ndipo awiriwa anayamba kumutsatira komanso kumuthandiza.+