-
2 Mbiri 5:4-6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Choncho akulu onse a Isiraeli anabwera ndipo Alevi ananyamula Likasa.+ 5 Iwo ananyamula Likasa, chihema chokumanako+ ndiponso ziwiya zonse zopatulika zimene zinali mʼchihemacho. Ansembe ndi Alevi* anabweretsa zinthuzi. 6 Mfumu Solomo ndi gulu lonse la Aisiraeli amene anawaitana, anasonkhana patsogolo pa Likasa. Iwo anapereka nsembe+ zosawerengeka za nkhosa ndi ngʼombe.
-