Levitiko 26:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndidzakuchititsani kuti musiye kunyada ndipo ndidzachititsa kumwamba kukhala ngati chitsulo+ ndi nthaka yanu ngati kopa.* Deuteronomo 28:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Thambo limene lili pamwamba pa mutu wanu lidzakhala ngati kopa,* ndipo nthaka yanu idzakhala ngati chitsulo.+
19 Ndidzakuchititsani kuti musiye kunyada ndipo ndidzachititsa kumwamba kukhala ngati chitsulo+ ndi nthaka yanu ngati kopa.*
23 Thambo limene lili pamwamba pa mutu wanu lidzakhala ngati kopa,* ndipo nthaka yanu idzakhala ngati chitsulo.+