1 Mafumu 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Makapu onse a Mfumu Solomo anali agolide, ndipo ziwiya zonse zamʼnyumba yotchedwa Nkhalango ya Lebanoni+ zinali zagolide yekhayekha. Panalibe chiwiya chasiliva chifukwa siliva sankaoneka ngati kanthu mʼmasiku a Solomo.+
21 Makapu onse a Mfumu Solomo anali agolide, ndipo ziwiya zonse zamʼnyumba yotchedwa Nkhalango ya Lebanoni+ zinali zagolide yekhayekha. Panalibe chiwiya chasiliva chifukwa siliva sankaoneka ngati kanthu mʼmasiku a Solomo.+