1 Mafumu 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ahisara anali woyangʼanira banja lachifumu, ndipo Adoniramu+ mwana wa Abada ankayangʼanira anthu olembedwa ntchito yokakamiza.+ 1 Mafumu 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mfumu Solomo inalemba amuna kuchokera ku Isiraeli konse kuti azigwira ntchito yokakamiza, ndipo anthu amene anawalembawo analipo 30,000.+
6 Ahisara anali woyangʼanira banja lachifumu, ndipo Adoniramu+ mwana wa Abada ankayangʼanira anthu olembedwa ntchito yokakamiza.+
13 Mfumu Solomo inalemba amuna kuchokera ku Isiraeli konse kuti azigwira ntchito yokakamiza, ndipo anthu amene anawalembawo analipo 30,000.+