1 Mafumu 11:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Atatero, anauza Yerobowamu kuti: “Tengapo mapisi 10, chifukwa Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ndikungʼamba ufumuwu kuuchotsa mʼmanja mwa Solomo ndipo iwe ndidzakupatsa mafuko 10.+
31 Atatero, anauza Yerobowamu kuti: “Tengapo mapisi 10, chifukwa Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ndikungʼamba ufumuwu kuuchotsa mʼmanja mwa Solomo ndipo iwe ndidzakupatsa mafuko 10.+