2 Mbiri 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Yehu+ mwana wa Haneni+ wamasomphenya, anapita kwa Mfumu Yehosafati ndipo anamufunsa kuti: “Kodi muyenera kuthandiza anthu oipa,+ ndipo kodi muyenera kukonda anthu odana ndi Yehova?+ Chifukwa cha zimenezi Yehova wakukwiyirani. 2 Mbiri 20:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Nkhani zina zokhudza Yehosafati, kuyambira pachiyambi mpaka pamapeto, zikupezeka mʼzinthu zimene Yehu+ mwana wa Haneni+ analemba ndipo zinaphatikizidwa mʼBuku la Mafumu a Isiraeli.
2 Ndiyeno Yehu+ mwana wa Haneni+ wamasomphenya, anapita kwa Mfumu Yehosafati ndipo anamufunsa kuti: “Kodi muyenera kuthandiza anthu oipa,+ ndipo kodi muyenera kukonda anthu odana ndi Yehova?+ Chifukwa cha zimenezi Yehova wakukwiyirani.
34 Nkhani zina zokhudza Yehosafati, kuyambira pachiyambi mpaka pamapeto, zikupezeka mʼzinthu zimene Yehu+ mwana wa Haneni+ analemba ndipo zinaphatikizidwa mʼBuku la Mafumu a Isiraeli.