2 Mafumu 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako Yehu anatumiza uthenga ku Isiraeli konse, moti anthu onse olambira Baala anabwera. Palibe amene sanabwere. Iwo analowa mʼkachisi wa Baala+ ndipo kachisiyo anadzaza kuchokera kutsogolo mpaka kumbuyo. 2 Mafumu 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Anagwetsa chipilala chopatulika+ cha Baala ndi kachisi wa Baala+ ndipo malowo anawasandutsa zimbudzi mpaka lero.
21 Kenako Yehu anatumiza uthenga ku Isiraeli konse, moti anthu onse olambira Baala anabwera. Palibe amene sanabwere. Iwo analowa mʼkachisi wa Baala+ ndipo kachisiyo anadzaza kuchokera kutsogolo mpaka kumbuyo.
27 Anagwetsa chipilala chopatulika+ cha Baala ndi kachisi wa Baala+ ndipo malowo anawasandutsa zimbudzi mpaka lero.