Yoswa 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pa nthawiyo Yoswa analumbira* kuti: “Munthu amene adzamangenso mzinda wa Yerikowu adzakhale wotembereredwa pamaso pa Yehova. Akadzangoyala maziko ake, mwana wake woyamba adzafe, ndipo akadzaika zitseko zapageti, mwana wake wotsiriza adzafe.”+
26 Pa nthawiyo Yoswa analumbira* kuti: “Munthu amene adzamangenso mzinda wa Yerikowu adzakhale wotembereredwa pamaso pa Yehova. Akadzangoyala maziko ake, mwana wake woyamba adzafe, ndipo akadzaika zitseko zapageti, mwana wake wotsiriza adzafe.”+