Luka 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mwachitsanzo, ndithu ndikukuuzani kuti: Munali akazi ambiri amasiye mu Isiraeli mʼmasiku a Eliya, pamene kumwamba kunatsekedwa kwa zaka zitatu ndi miyezi 6 ndipo mʼdziko lonse munali njala yaikulu.+ Yakobo 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Eliya anali munthu ngati ife tomwe, komabe atapemphera kuchokera pansi pamtima kuti mvula isagwe, mvula sinagwedi mʼdzikolo kwa zaka zitatu ndi miyezi 6.+
25 Mwachitsanzo, ndithu ndikukuuzani kuti: Munali akazi ambiri amasiye mu Isiraeli mʼmasiku a Eliya, pamene kumwamba kunatsekedwa kwa zaka zitatu ndi miyezi 6 ndipo mʼdziko lonse munali njala yaikulu.+
17 Eliya anali munthu ngati ife tomwe, komabe atapemphera kuchokera pansi pamtima kuti mvula isagwe, mvula sinagwedi mʼdzikolo kwa zaka zitatu ndi miyezi 6.+