Numeri 16:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno Mose anati: “Mudziwira izi kuti Yehova ndi amene wandituma kuti ndichite zonsezi, ndiponso kuti si zamʼmaganizo mwanga:* Yohane 11:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Inde, ndikudziwa kuti mumandimva nthawi zonse, koma ndikunena izi chifukwa cha gulu la anthu amene aimirira panowa, kuti akhulupirire kuti inu munandituma ine.”+
28 Ndiyeno Mose anati: “Mudziwira izi kuti Yehova ndi amene wandituma kuti ndichite zonsezi, ndiponso kuti si zamʼmaganizo mwanga:*
42 Inde, ndikudziwa kuti mumandimva nthawi zonse, koma ndikunena izi chifukwa cha gulu la anthu amene aimirira panowa, kuti akhulupirire kuti inu munandituma ine.”+