-
1 Mafumu 18:23, 24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Iwowo apeze ngʼombe zamphongo ziwiri zingʼonozingʼono. Asankhepo ngʼombe imodzi nʼkuiduladula. Ndiyeno aiike pankhuni koma asayatsepo moto. Ineyo ndikonza ngʼombe inayo nʼkuiika pankhuni, ndipo nanenso sindiyatsapo moto. 24 Kenako muitane dzina la mulungu wanu.+ Inenso ndiitana dzina la Yehova, ndipo Mulungu amene ayankhe potumiza moto asonyeza kuti ndi Mulungu woona.”+ Anthu onsewo atamva zimenezi anayankha kuti: “Zili bwino.”
-