-
Ekisodo 20:4, 5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Musadzipangire fano kapena chifaniziro cha chinthu chilichonse chakumwamba kapena chapadziko lapansi, kapenanso chamʼmadzi apadziko lapansi.+ 5 Musaziweramire kapena kuzitumikira,+ chifukwa ine Yehova Mulungu wanu, ndine Mulungu amene ndimafuna kuti anthu azidzipereka kwa ine ndekha,+ amene ndimalanga ana, zidzukulu ndi ana a zidzukuluzo, chifukwa cha zolakwa za abambo a anthu odana ndi ine.
-