-
1 Mafumu 1:51, 52Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
51 Solomo anauzidwa kuti: “Adoniya akuchita mantha ndi inu Mfumu Solomo moti wakagwira nyanga za guwa lansembe, ndipo wanena kuti, ‘Mfumu Solomo andilumbirire kaye ine mtumiki wake kuti sandipha ndi lupanga.’” 52 Solomo anayankha kuti: “Akamachita zabwino, tsitsi lake ngakhale limodzi silidzagwera pansi, koma akadzapezeka atachita choipa,+ adzaphedwa.”
-