2 Pa nthawi imeneyi Ahaziya ali mʼnyumba yake ku Samariya, anagwa kuchokera pachipinda chapadenga kudzera pachibowo chotchinga ndipo anavulala. Ndiyeno anatuma anthu kuti: “Pitani kwa Baala-zebabu mulungu wa ku Ekironi,+ mukafunse ngati ndingachire.”+