2 Mafumu 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma Elisa anati: “Ndikulumbira mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo amene ndimamutumikira, sindilandira.”+ Namani anamukakamiza kuti alandire, koma iye anakanabe.
16 Koma Elisa anati: “Ndikulumbira mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo amene ndimamutumikira, sindilandira.”+ Namani anamukakamiza kuti alandire, koma iye anakanabe.