1 Mafumu 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako Yehova anamuuza kuti: “Bwerera ndipo upite kuchipululu cha Damasiko. Ukakafika ukadzoze Hazaeli+ kuti akhale mfumu ya Siriya. 2 Mafumu 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsiku lotsatira, Hazaeli anatenga chofunda nʼkuchiviika mʼmadzi kenako anaphimba mfumuyo kumaso mpaka inamwalira.+ Ndiyeno Hazaeli anayamba kulamulira mʼmalo mwake.+ 2 Mafumu 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mʼmasiku amenewo, Yehova anayamba kuchepetsa dziko la Isiraeli pangʼono ndi pangʼono. Ndipo Hazaeli anapitiriza kuukira Aisiraeli mʼmadera awo onse.+
15 Kenako Yehova anamuuza kuti: “Bwerera ndipo upite kuchipululu cha Damasiko. Ukakafika ukadzoze Hazaeli+ kuti akhale mfumu ya Siriya.
15 Tsiku lotsatira, Hazaeli anatenga chofunda nʼkuchiviika mʼmadzi kenako anaphimba mfumuyo kumaso mpaka inamwalira.+ Ndiyeno Hazaeli anayamba kulamulira mʼmalo mwake.+
32 Mʼmasiku amenewo, Yehova anayamba kuchepetsa dziko la Isiraeli pangʼono ndi pangʼono. Ndipo Hazaeli anapitiriza kuukira Aisiraeli mʼmadera awo onse.+