1 Mafumu 21:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Kodi waona mmene Ahabu wadzichepetsera pamaso panga?+ Chifukwa wadzichepetsa pamaso panga, sindidzabweretsa tsokali iye adakali moyo. Mʼmalomwake, ndidzalibweretsa kwa anthu a mʼnyumba yake mʼnthawi ya mwana wake.”+
29 “Kodi waona mmene Ahabu wadzichepetsera pamaso panga?+ Chifukwa wadzichepetsa pamaso panga, sindidzabweretsa tsokali iye adakali moyo. Mʼmalomwake, ndidzalibweretsa kwa anthu a mʼnyumba yake mʼnthawi ya mwana wake.”+