-
Luka 1:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Komanso adzatsogola monga kalambulabwalo wa Mulungu ali ndi mzimu ndi mphamvu ngati za Eliya.+ Iye adzatembenuza mitima ya abambo kuti ikhale ngati ya ana+ ndipo anthu osamvera adzawatembenuzira ku nzeru yeniyeni ya anthu olungama. Adzachita zimenezi kuti asonkhanitse anthu amene akonzekera kutumikira Yehova.”*+
-