2 Mafumu 10:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Komabe iye sanasiye kuchita machimo amene Aisiraeli ankachita chifukwa cha Yerobowamu mwana wa Nebati. Machimo ake anali akuti sanachotse mwana wa ngʼombe wagolide amene anali ku Beteli komanso amene anali ku Dani.+ 2 Mafumu 17:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anangʼamba Isiraeli kumusiyanitsa ndi nyumba ya Davide ndipo iwo anaveka ufumu Yerobowamu mwana wa Nebati.+ Yerobowamuyo anasocheretsa Aisiraeli kuti asiye kutsatira Yehova nʼkuwachititsa tchimo lalikulu.
29 Komabe iye sanasiye kuchita machimo amene Aisiraeli ankachita chifukwa cha Yerobowamu mwana wa Nebati. Machimo ake anali akuti sanachotse mwana wa ngʼombe wagolide amene anali ku Beteli komanso amene anali ku Dani.+
21 Anangʼamba Isiraeli kumusiyanitsa ndi nyumba ya Davide ndipo iwo anaveka ufumu Yerobowamu mwana wa Nebati.+ Yerobowamuyo anasocheretsa Aisiraeli kuti asiye kutsatira Yehova nʼkuwachititsa tchimo lalikulu.