1 Awa ndi mawu a Amosi amene anali mmodzi wa anthu oweta nkhosa ku Tekowa.+ Anauzidwa mawu amenewa mʼmasomphenya okhudza Isiraeli, mʼmasiku a Uziya+ mfumu ya Yuda ndi mʼmasiku a Yerobowamu+ mwana wa Yowasi,+ mfumu ya Isiraeli, kutatsala zaka ziwiri kuti chivomerezi chichitike.+