2 Mbiri 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kenako anthu onse a ku Yuda anatenga Uziya,+ yemwe pa nthawiyo anali ndi zaka 16, nʼkumuika kuti akhale mfumu mʼmalo mwa bambo ake Amaziya.+ 2 Mbiri 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uziya+ anakhala mfumu ali ndi zaka 16, ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 52. Amayi ake anali a ku Yerusalemu ndipo dzina lawo linali Yekoliya.+
26 Kenako anthu onse a ku Yuda anatenga Uziya,+ yemwe pa nthawiyo anali ndi zaka 16, nʼkumuika kuti akhale mfumu mʼmalo mwa bambo ake Amaziya.+
3 Uziya+ anakhala mfumu ali ndi zaka 16, ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 52. Amayi ake anali a ku Yerusalemu ndipo dzina lawo linali Yekoliya.+