-
Levitiko 13:45, 46Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
45 Munthu amene ali ndi khateyo, zovala zake zizingʼambidwa ndipo asamakonze tsitsi lake. Koma aziphimba ndevu zake zapamlomo nʼkumafuula kuti, ‘Wodetsedwa, wodetsedwa!’ 46 Azikhala wodetsedwa pa nthawi yonse imene akudwala nthendayo. Chifukwa chakuti ndi wodetsedwa, azikhala kwayekha. Azikhala kunja kwa msasa.+
-