2 Mafumu 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako anthu onse a ku Yuda anatenga Azariya,*+ yemwe pa nthawiyo anali ndi zaka 16,+ nʼkumuika kuti akhale mfumu mʼmalo mwa bambo ake Amaziya.+
21 Kenako anthu onse a ku Yuda anatenga Azariya,*+ yemwe pa nthawiyo anali ndi zaka 16,+ nʼkumuika kuti akhale mfumu mʼmalo mwa bambo ake Amaziya.+