2 Mbiri 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kenako anthu onse a ku Yuda anatenga Uziya,+ yemwe pa nthawiyo anali ndi zaka 16, nʼkumuika kuti akhale mfumu mʼmalo mwa bambo ake Amaziya.+
26 Kenako anthu onse a ku Yuda anatenga Uziya,+ yemwe pa nthawiyo anali ndi zaka 16, nʼkumuika kuti akhale mfumu mʼmalo mwa bambo ake Amaziya.+