4 Ndidzatumiza moto panyumba ya Hazaeli,+
Ndipo udzawotcheratu nsanja zolimba za Beni-hadadi.+
5 Ndidzathyola mipiringidzo ya mageti a Damasiko.+
Ndidzapha anthu a ku Bikati-aveni,
Komanso wolamulira ku Beti-edeni.
Ndipo anthu a ku Siriya adzapita ku ukapolo ku Kiri,”+ watero Yehova.’