Ekisodo 34:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma maguwa awo ansembe mukawagwetse, zipilala zawo zopatulika mukaziphwanye ndipo mizati* yawo yopatulika mukaidule.+ Deuteronomo 16:21, 22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Musadzadzale mtengo uliwonse kuti ukhale mzati wopatulika*+ pafupi ndi guwa lansembe la Yehova Mulungu wanu limene mudzapange. 22 Ndipo musadzaimike chipilala chopatulika,+ chinthu chimene Yehova Mulungu wanu amadana nacho.”
13 Koma maguwa awo ansembe mukawagwetse, zipilala zawo zopatulika mukaziphwanye ndipo mizati* yawo yopatulika mukaidule.+
21 Musadzadzale mtengo uliwonse kuti ukhale mzati wopatulika*+ pafupi ndi guwa lansembe la Yehova Mulungu wanu limene mudzapange. 22 Ndipo musadzaimike chipilala chopatulika,+ chinthu chimene Yehova Mulungu wanu amadana nacho.”