Deuteronomo 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mukawonongeretu malo onse amene mitundu imene mukukailanda dziko lawo imatumikirirapo milungu yawo,+ kaya ndi pamapiri ataliatali, pazitunda ndi pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba obiriwira. Yesaya 57:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Amene mukukhala ndi chilakolako champhamvu chogonana pakati pa mitengo ikuluikulu,+Pansi pa mtengo uliwonse wa masamba ambiri?+Kodi si inu amene mumapha ana mʼzigwa,*+Pakati pa matanthwe?
2 Mukawonongeretu malo onse amene mitundu imene mukukailanda dziko lawo imatumikirirapo milungu yawo,+ kaya ndi pamapiri ataliatali, pazitunda ndi pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba obiriwira.
5 Amene mukukhala ndi chilakolako champhamvu chogonana pakati pa mitengo ikuluikulu,+Pansi pa mtengo uliwonse wa masamba ambiri?+Kodi si inu amene mumapha ana mʼzigwa,*+Pakati pa matanthwe?