Deuteronomo 1:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ngakhale kuti anakuchitirani zonsezi, simunakhulupirire Yehova Mulungu wanu,+ Deuteronomo 31:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ineyo ndikudziwa bwino khalidwe lanu lopanduka+ ndi kuuma mtima* kwanu.+ Ngati mwakhala mukupandukira Yehova pamene ndili moyo, ndiye kuli bwanji pambuyo pa imfa yanga!
27 Ineyo ndikudziwa bwino khalidwe lanu lopanduka+ ndi kuuma mtima* kwanu.+ Ngati mwakhala mukupandukira Yehova pamene ndili moyo, ndiye kuli bwanji pambuyo pa imfa yanga!