Deuteronomo 12:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 mukasamale kuti musakagwidwe mumsampha wawo, pambuyo poti awonongedwa ndi kuchotsedwa pamaso panu. Musakafunse zokhudza milungu yawo kuti, ‘Kodi mitundu imeneyi inkatumikira bwanji milungu yawo? Inenso ndichita zomwezo.’+
30 mukasamale kuti musakagwidwe mumsampha wawo, pambuyo poti awonongedwa ndi kuchotsedwa pamaso panu. Musakafunse zokhudza milungu yawo kuti, ‘Kodi mitundu imeneyi inkatumikira bwanji milungu yawo? Inenso ndichita zomwezo.’+