2 Mafumu 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iweyo wamva zimene mafumu a Asuri anachitira mayiko onse, kuti anawawononga.+ Ndiye iweyo ukuona ngati upulumuka? 2 Mafumu 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ili kuti mfumu ya Hamati, mfumu ya Aripadi ndiponso mfumu ya mzinda wa Sefaravaimu, wa Hena ndi wa Iva?’”+
11 Iweyo wamva zimene mafumu a Asuri anachitira mayiko onse, kuti anawawononga.+ Ndiye iweyo ukuona ngati upulumuka?
13 Ili kuti mfumu ya Hamati, mfumu ya Aripadi ndiponso mfumu ya mzinda wa Sefaravaimu, wa Hena ndi wa Iva?’”+