Deuteronomo 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova Mulungu wanu muzimuopa, muzimutumikira,+ muzikhala naye pafupi kwambiri komanso muzilumbira pa dzina lake. Yoswa 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma muyenera kumamatira Yehova Mulungu wanu+ ngati mmene mwakhala mukuchitira mpaka lero.
20 Yehova Mulungu wanu muzimuopa, muzimutumikira,+ muzikhala naye pafupi kwambiri komanso muzilumbira pa dzina lake.